NSANJA YA MLONDA Na. 1 2019 | Kodi Mulungu N’ndani?

Pezani mayankho pa mafunso 6 amene angakuthandizeni kukhala pa ubwenzi na Mulungu.

Kodi Mulungu N’ndani?

Kuti mukhale pa ubwenzi na Mulungu, cinthu coyamba ni kum’dziŵa bwino. Kodi mungacite motani zimenezo?

Kodi Dzina la Mulungu N’ndani?

Kodi mudziŵa kuti Mulungu ali na dzina imene imam’dziŵikitsa mwapadela?

Kodi Mulungu Ali na Makhalidwe Abwanji?

Kodi makhalidwe akulu-akulu a Mulungu ni ati?

Kodi Mulungu Waticitila Zotani?

Mungacite cidwi kudziŵa zimene Mulungu wacita pofuna kutsimikiza kuti anthu akhale na tsogolo labwino.

Kodi Mulungu Adzacita Ciani Kutsogolo?

Dziŵani mmene zinthu zidzakhalila m’boma lacilungamo la Mulungu.

Kodi Kum’dziŵa Bwino Mulungu Kungakupindulileni Bwanji?

Kodi amene ali pa ubwenzi na Mulungu akuyembekezela madalitso otani?

Mungakhale pa Ubwenzi na Mulungu

Onani njila zinayi zimene zingakuthandizeni kukhala pa ubwenzi na Mulungu.