Danieli: Citsanzo Cokhala Wokhulupilika kwa Moyo Wonse
Danieli: Citsanzo Cokhala Wokhulupilika kwa Moyo Wonse—Gawo 1
Kodi Danieli adzakhalabe wokhulupilika kwa Mulungu wake Yehova, pamene ali kutali na banja la kwawo, komanso mzinda wa kwawo uli matongwe?
Danieli: Citsanzo Cokhala Wokhulupilika kwa Moyo Wonse—Gawo 2
Ufumu wamphamvu utenga ulamulilo. Danieli ayang’ananizana na adani atsopano. Cikhulupililo cake ciyesedwa kuposa ni kale lonse.