Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

NYIMBO 17

‘Nifuna’

‘Nifuna’

(Luka 5:13)

  1. 1. Mwana wa Yehova M’lungu,

    Anaonetsa cikondi.

    Pobwela padziko Kutithandiza;

    Iye anadzipeleka.

    Anacilitsa

    odwala,

    Ogontha na osaona.

    Nchito yake anakwanilitsa

    Iye anati: ‘Nifuna.’

  2. 2. Tiyesetse kutengela,

    Yesu mu umoyo wathu.

    Pophunzitsa anthu, Kudziŵa M’lungu;

    Tikhale okoma mtima.

    Tithandize anthu onse,

    Akasoŵa zilizonse.

    Conco amasiye akapempha

    Tiyankhe kuti: ‘Nifuna.’

(Onaninso Yoh. 18:37; Aef. 3:19; Afil. 2:7.)