Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Unganidalile

Unganidalile

Daunilodi:

  1. 1. Nthawi zambili

    Yamatigwela masoka.

    Sitidziŵa zikanacitika

    Popanda masoka aya.

    M’lungu amaona

    Amatidziŵadi bwino,

    Adziŵa kuti tingapambanedi

    Ngati tasankha mwanzelu.

    (MWANA WA KOLASI)

    Amatikondadi

    Olo tili na mphatso zosiyana

    Afuna kuti’se

    Tizikonda monga iye.

    (KOLASI)

    Ndiwe mnzanga

    Umakhalapo, sumanisiya na pamavuto.

    Naine-

    Ukafuna thandizo pamavuto

    Nidzakhala mnzako

    Ungadalile.

  2. 2. Pa nthawi yolila

    Timatonthoza olila.

    Nthawi zina tingasoŵe zonena

    Timangogwetsa misozi.

    (MWANA WA KOLASI)

    Tikagwa m’mavuto

    Yehova akhoza kutilimbitsa.

    Naise tingathe

    Kuŵathandiza anzathu.

    (KOLASI)

    Ndiwe mnzanga

    Umakhalapo, sumanisiya na pamavuto.

    Naine-

    Ukafuna thandizo pamavuto

    Nidzakhala m’nzako

    Ungadalile.

    (KOLASI)

    Ndiwe mnzanga

    Umakhalapo, sumanisiya na pamavuto.

    Naine-

    Ukafuna thandizo pamavuto

    Nidzakhala m’nzako

    Ungadalile.