Mboni za Yehova Padziko Lonse

Albania

  • Gjirokastër, Albania​—Akupatsa munthu wina kabuku ka m’Chingelezi kakuti Was Life Created?

Mfundo Zachidule—Albania

  • 2,762,000—Chiwerengero cha anthu
  • 5,461—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 83—Mipingo
  • Pa anthu 511 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

ZOCHITIKA PA MOYO

Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Albania ndi ku Kosovo

Kodi anapeza madalitso otani omwe awathandiza kupirira ngakhale kuti akhala akukumana ndi mavuto?