Mboni za Yehova Padziko Lonse

Samoa

  • Apia, Samoa—Akuonetsa vidiyo ya chiyankhulo cha Samoa

Mfundo Zachidule—Samoa

  • 206,000—Chiwerengero cha anthu
  • 552—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 12—Mipingo
  • Pa anthu 392 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Tinapeza ‘Ngale Yamtengo Wapatali’

Werengani nkhani ya moyo wosangalala wa a Winston ndi a Pamela Payne a ku Australia.

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

“Zilumba Zambiri Zisangalale”

Werengani mbiri ya moyo wa Geoffrey Jackson, wa m’Bungwe Lolamulira.