Pitani ku nkhani yake

Zoti Muchite Pophunzira Baibulo

Muziyamikira Zinthu Zopatulika

Mungaphunzire zambiri pa nkhani ya Yakobo ndi Esau. Koperani nkhani ya m’Baibuloyi, iwerengeni, ndipo muiganizire mozama n’kuona mmene ingakuthandizireni.