Pitani ku nkhani yake

Inuyo Panokha Muzikonda Kwambiri Choonadi

Inuyo Panokha Muzikonda Kwambiri Choonadi

Tikhoza kukhala mabwenzi a Yehova ngati timakonda kwambiri choonadi. Tiyeni tione mmene tingachitire zimenezi.

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

KHALANI BWENZI LA YEHOVA

Inuyo Panokha Muzikonda Kwambiri Choonadi (Nyimbo 56)

Kodi mumakonda kwambiri choonadi?

ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA

Zoti Ana Achite

Gwiritsani ntchito zinthu zosangalatsa zimenezi, nkhani zochokera m’Baibulo komanso makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo pophunzitsa ana mfundo za m’Baibulo.