Pitani ku nkhani yake

Uzichita Zinthu Bwino Muutumiki

Uzichita Zinthu Bwino Muutumiki

Kodi mungathandize Kalebe ndi Sofiya kuti azichita zinthu bwino muutumiki?

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

KHALANI BWENZI LA YEHOVA

Uzichita Zinthu Bwino Muutumiki

Usanapite muutumiki, pali zinthu zitatu zimene uyenera kuzidziwa.

ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA

Zoti Ana Achite

Gwiritsani ntchito zinthu zosangalatsa zimenezi, nkhani zochokera m’Baibulo komanso makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo pophunzitsa ana mfundo za m’Baibulo.