Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

NYIMBO 98

Malemba ni Ouzilidwa na Mulungu

Malemba ni Ouzilidwa na Mulungu

(2 Timoteyo 3:16, 17)

  1. 1. Mu dziko ili la mdima,

    Timaona kuwala,

    Kwa Mau a M’lungu wathu,

    Opezeka mu Baibo.

  2. 2. Yehova anatipatsa

    Mau ouzilidwa.

    Kuti atitsogolele

    Mu njila ya cilungamo.

  3. 3. Mau a Yehova M’lungu

    Amatilimbikitsa.

    Iye ni Atate wathu,

    Tidziŵa amatikonda.

(Onaninso Sal. 119:105; Miy. 4:13.)