Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kusonkhana Pamodzi Kumatithandiza

Kusonkhana Pamodzi Kumatithandiza

Hezekiya anakonza mwambo wa Pasika ku Yerusalemu (2Mb 30:1; it-1 1103 ¶2)

Anthu ambiri anapezeka pamwambowu ngakhale ankatsutsidwa (2Mb 30:10, 11, 13; it-1 1103 ¶3)

Iwo anasangalala kwambiri ndipo analimbikitsidwa kuti azilambira Yehova (2Mb 30:25–31:1; it-1 1103 ¶4-5)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi kupezeka pamisonkhano yampingo komanso ikuluikulu pamasom’pamaso kwandithandiza bwanji ngakhale kuti ndimakumana ndi mavuto ena?’