Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Khulupirirani Yehova Mulungu Wanu”

“Khulupirirani Yehova Mulungu Wanu”

Yehosafati limodzi ndi anthu a ku Yuda ataopsezedwa, anapempha Yehova kuti awathandize (2Mb 20:12, 13; w14 12/15 23 ¶8)

Yehova analimbikitsa anthu ake ndipo anawapatsa malangizo omveka bwino (2Mb 20:17)

Yehova anapulumutsa anthu ake chifukwa anamukhulupirira (2Mb 20:21, 22, 27; w21.11 16 ¶7)

Gogi akadzaukira anthu a Mulungu pa chisautso chachikulu, anthu amene amakhulupirira Yehova komanso kudalira anthu amene iye anawasankha kuti azititsogolera, sadzachita mantha.​—2Mb 20:20