Nkhani Zina

Pamalowa mungapezepo nkhani zosiyanasiyana kuphatikizapo zomwe zili patsamba loyamba la jw.org. Werengani nkhani zimenezi komanso kuonera mavidiyo omwe alipo kuti mupeze nzeru zothandiza za m’Baibulo kuti mulimbitse chikhulupiriro chanu.

KHALANI MASO

Kodi Anthu Adzasiya Liti Kumenya Nkhondo?​—Zimene Baibulo Limanena

Posachedwapa nkhondo zonse zidzathetsedwa. Baibulo limafotokoza mmene zimenezi zidzachitikire.

Kuteteza Akazi—Zimene Baibulo Limanena

Mulungu amaona kuti akazi ayenera kutetezedwa. Onani chifukwa chake amaona choncho komanso zimene adzachite pothetsa nkhanza zonse zimene anthu amachitira akazi.

Muzithandiza Ena Kuti Musamasungulumwe​—Kodi Baibulo Limati Chiyani?

Onani njira ziwiri zimene mungachite kuti mupindule pothandiza anthu ena.

NTCHITO YOITANIRA ANTHU KU CHIKUMBUTSO

Yesu Adzathetsa Zoipa Zonse

Kodi tingasonyeze bwanji kuti timayamikira zimene Yesu watichitira kale komanso zimene adzatichitire?

NTCHITO YOITANIRA ANTHU KU CHIKUMBUTSO

Yesu Adzathetsa Umphawi

Kodi tingasonyeze bwanji kuti timayamikira zimene Yesu watichitira kale ndiponso zimene adzatichitire posachedwapa?

NTCHITO YOITANIRA ANTHU KU CHIKUMBUTSO

Yesu Adzathetsa Nkhondo

Kodi tingasonyeze bwanji kuyamikira zimene Yesu watichitira kale komanso zomwe adzatichitire posachedwapa?

KHALANI MASO

Ndalama Zambirimbiri Zikuthera Kunkhondo—Kodi Ndi Ndalama Zochuluka Bwanji?

Onani chifukwa chake padzikoli anthu sazidzagwiritsanso ntchito zinthu pa nkhondo komanso mmene nkhondo ndi mavuto ake zidzathere.

Pezani Anzanu Abwino Kuti Musamasungulumwe—Kodi Baibulo Lingakuthandizeni Bwanji?

Onani mfundo ziwiri za m’Baibulo zimene zingakuthandizeni kulimbana ndi vuto losungulumwa.

KHALANI MASO

Anthu Ayamba Kusiya Kukhulupirira Andale—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Baibulo limatilimbikitsa kuti tizisamala ndi anthu omwe timawakhulupirira ndipo limatiuza za njira yodalirika yomwe ingatithandize kukhala ndi tsogolo lowala.

KHALANI MASO!

Kodi Nkhondo Yapadziko Lonse Ichitika Posachedwapa?​—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Baibulo silinangolosera za nkhondo zochuluka zimene zikuchitika masiku ano basi, koma linaloseranso za mmene nkhondo zonse zidzathere.

Vuto Losungulumwa Padziko Lonse​—Kodi Mungalimbane Nalo Bwanji?

Taonani mfundo za m’Baibulo ziwiri zomwe zingakuthandizeni kulimbana ndi vuto losungulumwa.

Anthu Ambiri Akusungulumwa​—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Onani zimene zingathandize anthu amene akusungulumwa kuti ayambirenso kusangalala.

KHALANI MASO

N’chifukwa Chiyani Anthu Sangathe Kubweretsa Mtendere?​—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe chifukwa chake anthu sangathetse nkhondo.

KHALANI MASO!

Mungakhale Ndi Chiyembekezo Chabwino mu 2024—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Zimene Baibulo limalonjeza zingakuthandizeni kukhala moyo wabwino panopa komanso tsogolo labwino.

KHALANI MASO!

Chaka cha 2023 Chinali Chodetsa Nkhawa Kwambiri—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Baibulo limafotokoza tanthauzo la mavuto amene akhala akuchitika padzikoli mu chaka cha 2023.

KHALANI MASO

N’chifukwa Chiyani Anthu Akudana Kwambiri?​—⁠Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Dziwani chifukwa chake chidani chomwe chikuchitika padzikoli masiku ano chili ndi tanthauzo lofunika kwambiri komanso zimene Mulungu adzachite pa nkhani imeneyi.

KHALANI MASO

Ndi Ndani Angateteze Anthu Wamba Pankhondo?—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Baibulo linaneneratu kuti Mulungu ‘adzathetsa nkhondo padziko lonse lapansi.’ Kodi adzachita zimenezi motani?

KHALANI MASO

Kodi Aramagedo Idzayambira ku Isiraeli?—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Tingapeze yankho tikaona zomwe buku la Chivumbulutso limanena zokhudza Aramagedo.

Kodi Choonadi Ndi Chofunikabe Masiku Ano?

Baibulo lingakuthandizeni kudziwa choonadi m’dziko lomwe anthu ambiri akumafalitsa mabodza.

NTCHITO YAPADERA YOLALIKIRA

Mavuto Azachuma—Kodi Ufumu wa Mulungu Udzachita Zotani?

Kodi mukudziwa kuti Baibulo limanena kuti pali boma limene lidzathetse mavuto onse azachuma kuphatikizapo kusalana?

NTCHITO YAPADERA YOLALIKIRA

Mavuto Okhudza Zachilengedwe—Kodi Ufumu wa Mulungu Udzachita Zotani?

Onani zimene Ufumu wa Mulungu udzachite pothetsa mavuto onse okhudza chilengedwe padzikoli.

NTCHITO YAPADERA YOLALIKIRA

Thandizo la Zaumoyo—Kodi Ufumu wa Mulungu Udzachita Zotani?

Werengani magaziniyi kuti mudziwe zimene Ufumu wa Mulungu udzachite kuti anthufe tidzakhale ndi moyo wathanzi.

NTCHITO YAPADERA YOLALIKIRA

Nkhondo—Kodi Ufumu wa Mulungu Udzachita Zotani?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zimene Ufumu wa Mulungu udzachite kuti ubweretse mtendere weniweni komanso chitetezo.

Kodi Baibulo Limanena Zotani Zokhudza Kusowa kwa Chakudya Masiku Ano?

Mulungu si amene amachititsa kuti chakudya chizisowa, koma anatichenjezeratu zokhudza zimenezi.

KHALANI MASO

Madzi Osefukira—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Kodi madzi osefukira amene sanayambe achitikapo m’mbuyomu padziko lonse, akutiphunzitsa zotani zokhudza nthawi yathu ino?

KHALANI MASO

Vuto la Kusowa kwa Chakudya Padziko Lonse Chifukwa cha Nkhondo ndi Kusintha kwa Nyengo—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Baibulo silimangopereka malangizo othandiza okha koma limatipatsanso chiyembekezo kuti zinthu zidzakhala bwino m’tsogolo.

KHALANI MASO

Nyengo Yotentha Modabwitsa M’chaka cha 2023—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Baibulo limanen akuti Mulungu sadzalola kuti dziko lapansi liwonongedwe.

KHALANI MASO

Katswiri wa za Umoyo Wachenjeza Kuti Achinyamata Angakumane Ndi Mavuto Pamalo Ochezera a pa Intaneti—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Onani mfundo za m’Baibulo zitatu zimene zingathandize makolo kuteteza ana awo.

Mabuku a Uthenga Wabwino a Mateyu ndi Yohane Atulutsidwa M’Chinenero Chamanja cha ku Germany

Pa 18 December 2021, Mabuku a Uthenga Wabwino a Mateyu ndi Yohane anatulutsidwa m’Chinenero Chamanja cha ku Germany. Kameneka ndi koyamba kuti mabuku athunthu a m’Baibulo atulutsidwe m’chinenerochi.

KHALANI MASO

Kodi Nzeru Zopangidwa Ndi Anthu, N’zothandizadi Kapena Zingayambitse Mavuto?—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Baibulo limasonyeza chifukwa chake sitingadalire kuti zipangizo zamakono zimene anthu akupanga masiku ano zingachititse kuti zinthu ziziyenda bwino padzikoli

Zimene Tingachite Kuti Nsembe ya Yesu Izitithandiza

Kodi Yesu anatiphunzitsa zinthu zofunika ziwiri ziti zimene tiyenera kuchita kuti tipindule ndi imfa yake?

KHALANI MASO

Nkhondo ya ku Ukraine Ikulowa Chaka Chachiwiri—Kodi Baibulo Limapereka Chiyembekezo Chotani?

Phunzirani zokhudza lonjezo lopezeka m’Baibulo lakuti nkhondo zonse zidzatha.

KHALANI MASO

Achinyamata Ambiri Akuvutika Ndi Matenda Amaganizo—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Baibulo limapereka malangizo othandiza kwa achinyamata omwe akuvutika maganizo.

KHALANI MASO

Ku Turkey ndi ku Syria Kwachitika Zivomerezi Zoopsa—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Anthu amene akhudzidwa ndi zivomerezi ku Turkey ndi ku Syria angalimbikitsidwe ndi kutonthozedwa ndi zimene Baibulo limanena.

KHALANI MASO

Asayansi Asunthira Kutsogolo Wotchi Yosonyeza Nthawi ya Kutha kwa Dziko—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Ngakhale kuti Baibulo limanena za mapeto, komabe limatithandizanso kukhala ndi maganizo oyenerera.

KHALANI MASO

Kodi N’zotheka Kuti Anthu a Mitundu Yonse Azionedwa Mofanana?—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Anthu mamiliyoni akuphunzira kuchokera m’Baibulo mmene angamachitire zinthu mwa ulemu ndi ena.

KHALANI MASO

N’chifukwa Chiyani Ndale Zimagawanitsa Kwambiri Anthu?—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Padziko lonse, anthu ambiri sagwirizana pa nkhani za ndale. Baibulo linaneneratu njira yothetsera vutoli. Pali boma lolamuliridwa ndi winawake amene adzachotse mavuto onse omwe amapangitsa anthu kuti azivutika.

KHALANI MASO

Yambani Chaka cha 2023 Muli Ndi Chiyembekezo—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Anthu ambiri amakhala ndi chiyembekezo cha tsogolo lowala akangolowa m’chaka chatsopano. Uthenga wabwino wa m’Baibulo ungatithandize kukhala ndi tsogolo lowala.

KHALANI MASO

M’chaka cha 2022 Tinakumana Ndi Mavuto Ambiri​—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Baibulo lokha ndi limene lingatiuze zolondola zokhudza tanthauzo la zimene zachitika posachedwapa.

KHALANI MASO

Kodi Mpira wa World Cup Ungachititsedi Anthu Kukhala Ogwirizana?​—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Mpira wa World Cup wasonyeza kuti anthu aganizira zambiri osati mpira wokha.

KHALANI MASO

Kodi Mayiko Angagwirizane Pothana Ndi Vuto la Kusintha Kwa Nyengo?—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Baibulo linalosera molondola zimene zikulepheretsa mayiko kuthana ndi mavutowa.

Uthenga Wotonthoza Anthu Omwe Aferedwa

Munthu amene tinkamukonda akamwalira, tingaganize kuti palibe amene akutimvetsa mmene tikumvera. Koma Mulungu amatimvetsa ndipo ndi wokonzeka kuti atithandize.

KHALANI MASO

Kodi Mudzasankha Ndani Kukhala Mtsogoleri Wanu?—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Ngakhale olamulira ena amakhala abwino, koma ali ndi malire. Pali Mtsogoleri mmodzi yekha yemwe tingamudalire.

KHALANI MASO

Atsogoleri Andale Akuchenjeza za Aramagedo—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Kodi kugwiritsa ntchito zida za nyukiliya kungayambitse Aramagedo?

KHALANI MASO

Ng’amba Yoopsa—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Kodi vuto limeneli lidzathetsedwa bwanji? Nanga kodi tiyembekezere kuti zinthu zidzakhala bwino m’tsogolo?

KHALANI MASO

Kodi Akhristu Ayenera Kumenya Kapena Kuthandizira Nkhondo?—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Kodi Akhristu amene amamenya kapena kutenga mbali pa nkhondo amakhala akutsatira zimene Yesu ananena?

KHALANI MASO

Kunja Kukutentha Modetsa Nkhawa—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Kodi nthawi ina padzikoli sipadzapezekanso chamoyo chilichonse?

KHALANI MASO

Anthu Akuwononga Dziko Lapansi—Kodi Baibulo Limanena zotani?

Vesi lina la m’Baibulo limatchula zinthu zitatu zokhudza vuto la zachilengedwe lomwe lakhudza dziko lapansili.

KHALANI MASO

Kukwera Mitengo Kwa Zinthu Padziko Lonse—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

N’chifukwa chiyani tikukumana ndi mavuto azachuma? Kodi Baibulo lingatithandize bwanji?

KHALANI MASO

Kuwombera M’masukulu—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

N’chifukwa chiyani zinthu zoopsazi zimachitika? Kodi zinthu zachiwawa ngati zimenezi zingadzathedi?

KHALANI MASO

Nkhondo ya ku Ukraine Ikuwonjezera Vuto la Kuchepa Kwa Chakudya Padziko Lonse

Baibulo linaneneratu kale za mavuto a kusowa kwa chakudya. Komabe limatipatsa chiyembekezo komanso malangizo abwino omwe angatithandize polimbana ndi vutoli panopo.

KHALANI MASO

Anthu 6 Miliyoni Anamwalira ndi Matenda a COVID​—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Baibulo linaneneratu kuti kudzakhala miliri yoopsa, limatitonthoza kuti tipirire mavuto amenewa, komanso limatiuza njira imene Mulungu adzagwiritse ntchito kuti adzathetse vutoli mpaka kalekale.

Mfundo za M’Baibulo Zomwe Zingakuthandizeni Ngati Mwachotsedwa Ntchito

Phunzirani njira zokwanira 6 zomwe zingakuthandizeni.

Kodi Baibulo Linaneneratu Zotani pa Nkhani ya Zivomerezi Zamphamvu?

Werengani nkhaniyi kuti muone zivomerezi zina zamphamvu zomwe zachitika m’zaka zaposachedwa. Onaninso mmene maulosi a m’Baibulo akutithandizira kudziwa zomwe zikuyembekezeka kuchitika m’tsogolomu.

Kodi Katangale Adzatha M’Boma?

Onani zifukwa zitatu zomwe zikutitsimikizira za boma linalake lapadera kuti silidzachita zachinyengo.

KHALANI MASO

Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani Yopembedza Zizindikiro

Kodi Mulungu zimam’khudza ngati timagwiritsa ntchito mafano komanso ziboliboli popemphera?

KHALANI MASO

Zimene Zipembedzo Zikuchita pa Nkhondo ya ku Ukraine—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Kumbali zonse, atsogoleri amatchalitchi ali ndi maganizo osiyana kwambiri ndi zomwe Yesu anaphunzitsa otsatira ake kuti azichita komanso zoti asamachite.

KHALANI MASO

Anthu Ambirimbiri Athawa Nkhondo M’dziko la Ukraine

Baibulo limafotokoza zifukwa zenizeni zomwe zachititsa vutoli komanso mmene mavutowa adzathere mpaka kalekale.

Asilikari a Dziko la Russia Alowa M’dziko la Ukraine

Ngati ndi choncho, kodi Baibulo limafotokoza mmene zimenezi zithere?

Zomwe Baibulo Limanena pa Nkhani Yakusintha Kwa Nyengo Komanso Tsogolo Lathu

Kodi Mulungu amasamalako za anthufe komanso za dziko lomwe tikukhalapoli?

Kodi Moyo Udzabwereranso Mwakale?—Mmene Baibulo Lingakuthandizireni M’nthawi ya Mliri

Mfundo 6 za m’Baibulo zingatithandize kudziwa zoyenera kuchita komanso kupirira mavuto omwe akubwera m’tsogolomu.

Kodi Zipembedzo Ziyenera Kuchita Nawo Zandale?

Padziko lonse, anthu omwe amati ndi otsatira a Yesu Khristu amalowerera kwambiri munkhani zandale. Kodi ayeneradi kumachita zimenezi?

Kodi Mayiko Angathe Kuyendetsa Chuma Mokomera Aliyense?

Pali boma limene lingathe kulamulira dziko lapansi m’njira yabwino kwambiri, n’kuthetseratu umphawi ndi mavuto azachuma.

Kodi Baibulo Lingakuthandizeni Pakachitika Ngozi Zam’chilengedwe?

Malangizo a m’Baibulo angakuthandizeni pasanachitike ngozi zam’chilengedwe, pamene zikuchitika komanso pambuyo pake.

Kodi Uchigawenga Udzatha?

Mpaka nthawi imene zonse zochititsa mantha komanso zachiwawa zidzathe, zinthu ziwiri zimene Baibulo limatilimbikitsa kuchita zingathandize anthu omwe akhudzidwa ndi zauchigawenga.

Kodi Dzikoli Lidzatha? Kodi Baibulo Limanena Kuti Zinthu Zonse Zidzawonongedwa?

Ngakhale kuti Baibulo limanena kuti dzikoli lidzakhala mpaka kalekale, pali dziko limene lidzathe.

Samalani Kuti Musamapusitsike Ndi Nkhani Zabodza

Nkhani zosocheretsa, malipoti abodza ndi mphekesera zafala kwambiri ndipo zingakubweretsereni mavuto.

Zimene Mungachite Mukaferedwa

Muone zinthu zimene zingakuthandizeni kupirira.

Kodi Tingatani Kuti Tisamade Nkhawa Kwambiri?

Kodi ndi mavesi a m’Baibulo ati komanso zinthu ziti zimene zingakuthandizeni kuti musamade nkhawa kwambiri?

Tiziyembekezera Kuti Zinthu Zidzakhala Bwino M’tsogolo

N’chifukwa chiyani tinganene kuti malonjezo a m’Baibulo ndi osiyana ndi malonjezo komanso maganizo a anthu?

Kodi Chipembedzo Chasanduka Bizinezi Yotentha?

Nthawi zina anthu amene amabwera kutchalitchi ndi osauka, pomwe m’busa wa tchalitchicho ndi wolemera kwambiri.

Kodi Ndi Ndani Amene Adzapulumutse Dzikoli?

Akatswiri ena a chilengedwe amanena kuti zimene anthu akuchita panopa zikhoza kuwonongeratu mitundu ina ya zinyama ndi zitsamba.

Baibulo Lingathandize Amuna Amene Ali Ndi Nkhawa

Nkhawa ndi vuto lalikulu kwambiri popeza tili munthawi yapadera komanso yovuta, ndiye kodi Baibulo lingakuthandizeni?

Zimene Zingatithandize Ngati Tatopa ndi Mliri

Ngati sitichita zinthu zimene zingatithandize kuti tisatope ndi mliriwu, pang’ono ndi pang’ono tingayambe kugwa ulesi pa nkhani yotsatira malangizo otitetezera ku COVID-19.

Kodi Zinthu Zopanda Chilungamo Zidzatha Padzikoli?

Baibulo limasonyeza kuti chilungamo chenicheni chimachokera kwa Mulungu amene amaona kuti moyo wa munthu aliyense ndi wofunika.

Baibulo la Dziko Latsopano Lokonzedwanso Linatulutsidwa M’Chisipanishi

Kodi omasulira Baibulo anakwanitsa bwanji kumasulira Baibulo limene mawu amodzi amatanthauza zinthu zingapo m’madera ena apadziko lapansi?

Zimene Zingakuthandizeni Ngati Mwayamba Kudwala Mwadzidzidzi

Kodi ndi mfundo ziti za m’Baibulo zimene zingakuthandizeni ngati mwayamba kudwala mosayembekezereka?

Zimene Mungachite Ngati Mukupeza Ndalama Zochepa

Mavuto azachuma akabwera mwadzidzidzi zimadetsa nkhawa, koma mfundo za m’Baibulo zingakuthandizeni kuti muzitha kugwiritsa ntchito ndalama zochepa.

Mungatani Kuti Musayambe Kumwa Mowa Mopitirira Malire?

Mfundo 5 zimene zingakuthandizeni kuti musamamwe mowa mopitirira malire ngakhale pamene muli ndi nkhawa kwambiri.

Mfundo Zothandiza Anthu Omwe Achitiridwa Nkhanza Zosiyanasiyana

Dziwani kuti wolakwa si inuyo ndipo sikuti muli nokha.

Zimene Mungachite Ngati Muli Nokhanokha

Mukamamva kuti muli nokhanokha, mungayambe kuona kuti simungathe kupeza chiyembekezo, chimwemwe komanso kukhala wokhutira​—komatu si choncho.

Kodi Yohane M’batizi Anakhalapodi?

Katswiri wolemba mbiri yakale dzina lake Josephus anatsimikizira mfundo yakuti Yohane M’batizi anakhalapodi. Choncho ifenso tiyenera kukhulupirira mfundo imeneyi.

Zolemba Zakale Zimatsimikizira za Malo Amene Aisiraeli Ankakhala

Mapale a ku Samariya amasonyeza kuti zomwe Baibulo limanena zokhudza mbiri yakale ndi zoona.

Kodi Zidindo Zakale Zinkagwira Ntchito Yanji?

N’chifukwa chiyani zidindo zakale zinali zofunika, nanga olamulira ankazigwiritsa ntchito bwanji?

Kodi Zimene Baibulo Limanena Zokhudza Ukapolo wa Ayuda ku Babulo N’zolondola?

Kodi zimene akatswiri ofufuza anapeza zikugwirizana bwanji ndi zimene Mulungu ananena zokhudza moyo wa Ayuda ali ku ukapolo ku Babulo?

Chipilala Chakale cha ku Iguputo Chili Ndi Umboni wa Nkhani ya M’Baibulo

Werengani nkhaniyi kuti muone mmene zolemba zakale za ku Iguputo zimasonyezera kuti anthu omwe analemba Baibulo anali oona mtima.

Mulungu Anapereka Mfundo Zokhudza Ukhondo Asayansi Asanazitulukire

Aisiraeli zinthu zinkawayendera bwino chifukwa chotsatira malangizo a Mulungu okhudza ukhondo.

Zimene Asayansi Afukula Zikutsimikizira Kuti Mfumu Davide Analikodi

Anthu ena amanena kuti Mfumu Davide kunalibe ndipo nkhani yake ndi yongopeka. Kodi asayansi apeza umboni wotani?

Dzina la Mulungu Limapezekanso mu Mpukutu Wakale

Onani umboni wosonyeza kuti dzina la Mulungu linkapezeka mu “Chipangano Chatsopano.”

Njira Zothandiza Powerenga Baibulo

Ndandandayi ingakuthandizeni kwambiri kaya mukufuna kumangowerenga Baibulo tsiku lililonse, kukhala ndi cholinga chomaliza kuwerenga Baibulo chaka chimodzi kapena kutsatira ndondomeko yowerengera Baibulo ya anthu omwe angoyamba kumene.

Kodi Moyo Unayamba Bwanji?

Zoona zake n’zakuti pali anthu ambiri ophunzira kuphatikizapo asayansi ena omwe amakayikira zoti zamoyo zinachita kusintha kuchokera ku zinthu zina.

Mmene Mungapezere Malemba M’Baibulo Lanu

Mndandanda wa mabuku 66 a m’Baibulo ndipo aikidwa mmene aliri m’Mabaibulo ambiri. Dzina la buku lalembedwa koyambirira kenako chaputala ndipo pomaliza vesi lake.

Ankalemekeza Kwambiri Baibulo

William Tyndale komanso Michael Servetus ali m’gulu la anthu omwe ankatsutsidwa komanso kuopsezedwa kuti aphedwa. Iwo analolera kuika moyo wawo pangozi n’cholinga chofuna kuteteza choonadi cha m’Baibulo.

Ankalemekeza Kwambiri Baibulo—Kachigawo ka Vidiyo (William Tyndale)

Umboni wakuti ankakonda kwambiri Baibulo umaonekera mu ntchito imene anagwira imene imatithandizabe masiku ano.

TSAMBA LOYAMBA

Kuteteza Akazi—Zimene Baibulo Limanena

Mulungu amaona kuti akazi ayenera kutetezedwa. Onani chifukwa chake amaona choncho komanso zimene adzachite pothetsa nkhanza zonse zimene anthu amachitira akazi.

Muzithandiza Ena Kuti Musamasungulumwe​—Kodi Baibulo Limati Chiyani?

Onani njira ziwiri zimene mungachite kuti mupindule pothandiza anthu ena.

NTCHITO YOITANIRA ANTHU KU CHIKUMBUTSO

Yesu Adzathetsa Zoipa Zonse

Kodi tingasonyeze bwanji kuti timayamikira zimene Yesu watichitira kale komanso zimene adzatichitire?

NTCHITO YOITANIRA ANTHU KU CHIKUMBUTSO

Yesu Adzathetsa Umphawi

Kodi tingasonyeze bwanji kuti timayamikira zimene Yesu watichitira kale ndiponso zimene adzatichitire posachedwapa?

NTCHITO YOITANIRA ANTHU KU CHIKUMBUTSO

Yesu Adzathetsa Nkhondo

Kodi tingasonyeze bwanji kuyamikira zimene Yesu watichitira kale komanso zomwe adzatichitire posachedwapa?

Pezani Anzanu Abwino Kuti Musamasungulumwe—Kodi Baibulo Lingakuthandizeni Bwanji?

Onani mfundo ziwiri za m’Baibulo zimene zingakuthandizeni kulimbana ndi vuto losungulumwa.

Anthu Ambiri Akusungulumwa​—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Onani zimene zingathandize anthu amene akusungulumwa kuti ayambirenso kusangalala.

Vuto Losungulumwa Padziko Lonse​—Kodi Mungalimbane Nalo Bwanji?

Taonani mfundo za m’Baibulo ziwiri zomwe zingakuthandizeni kulimbana ndi vuto losungulumwa.

Kodi Choonadi Ndi Chofunikabe Masiku Ano?

Baibulo lingakuthandizeni kudziwa choonadi m’dziko lomwe anthu ambiri akumafalitsa mabodza.

NTCHITO YAPADERA YOLALIKIRA

Mavuto Azachuma—Kodi Ufumu wa Mulungu Udzachita Zotani?

Kodi mukudziwa kuti Baibulo limanena kuti pali boma limene lidzathetse mavuto onse azachuma kuphatikizapo kusalana?

NTCHITO YAPADERA YOLALIKIRA

Mavuto Okhudza Zachilengedwe—Kodi Ufumu wa Mulungu Udzachita Zotani?

Onani zimene Ufumu wa Mulungu udzachite pothetsa mavuto onse okhudza chilengedwe padzikoli.

NTCHITO YAPADERA YOLALIKIRA

Thandizo la Zaumoyo—Kodi Ufumu wa Mulungu Udzachita Zotani?

Werengani magaziniyi kuti mudziwe zimene Ufumu wa Mulungu udzachite kuti anthufe tidzakhale ndi moyo wathanzi.

NTCHITO YAPADERA YOLALIKIRA

Nkhondo—Kodi Ufumu wa Mulungu Udzachita Zotani?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zimene Ufumu wa Mulungu udzachite kuti ubweretse mtendere weniweni komanso chitetezo.

Kodi Baibulo Limanena Zotani Zokhudza Kusowa kwa Chakudya Masiku Ano?

Mulungu si amene amachititsa kuti chakudya chizisowa, koma anatichenjezeratu zokhudza zimenezi.

Mfundo za M’Baibulo Zomwe Zingakuthandizeni Ngati Mwachotsedwa Ntchito

Phunzirani njira zokwanira 6 zomwe zingakuthandizeni.

Kodi Baibulo Linaneneratu Zotani pa Nkhani ya Zivomerezi Zamphamvu?

Werengani nkhaniyi kuti muone zivomerezi zina zamphamvu zomwe zachitika m’zaka zaposachedwa. Onaninso mmene maulosi a m’Baibulo akutithandizira kudziwa zomwe zikuyembekezeka kuchitika m’tsogolomu.

Kodi Katangale Adzatha M’Boma?

Onani zifukwa zitatu zomwe zikutitsimikizira za boma linalake lapadera kuti silidzachita zachinyengo.

Zomwe Baibulo Limanena pa Nkhani Yakusintha Kwa Nyengo Komanso Tsogolo Lathu

Kodi Mulungu amasamalako za anthufe komanso za dziko lomwe tikukhalapoli?

Kodi Moyo Udzabwereranso Mwakale?—Mmene Baibulo Lingakuthandizireni M’nthawi ya Mliri

Mfundo 6 za m’Baibulo zingatithandize kudziwa zoyenera kuchita komanso kupirira mavuto omwe akubwera m’tsogolomu.

Kodi Zipembedzo Ziyenera Kuchita Nawo Zandale?

Padziko lonse, anthu omwe amati ndi otsatira a Yesu Khristu amalowerera kwambiri munkhani zandale. Kodi ayeneradi kumachita zimenezi?

Kodi Mayiko Angathe Kuyendetsa Chuma Mokomera Aliyense?

Pali boma limene lingathe kulamulira dziko lapansi m’njira yabwino kwambiri, n’kuthetseratu umphawi ndi mavuto azachuma.

Kodi Baibulo Lingakuthandizeni Pakachitika Ngozi Zam’chilengedwe?

Malangizo a m’Baibulo angakuthandizeni pasanachitike ngozi zam’chilengedwe, pamene zikuchitika komanso pambuyo pake.

Kodi Uchigawenga Udzatha?

Mpaka nthawi imene zonse zochititsa mantha komanso zachiwawa zidzathe, zinthu ziwiri zimene Baibulo limatilimbikitsa kuchita zingathandize anthu omwe akhudzidwa ndi zauchigawenga.

Kodi Dzikoli Lidzatha? Kodi Baibulo Limanena Kuti Zinthu Zonse Zidzawonongedwa?

Ngakhale kuti Baibulo limanena kuti dzikoli lidzakhala mpaka kalekale, pali dziko limene lidzathe.

Samalani Kuti Musamapusitsike Ndi Nkhani Zabodza

Nkhani zosocheretsa, malipoti abodza ndi mphekesera zafala kwambiri ndipo zingakubweretsereni mavuto.

Kodi Tingatani Kuti Tisamade Nkhawa Kwambiri?

Kodi ndi mavesi a m’Baibulo ati komanso zinthu ziti zimene zingakuthandizeni kuti musamade nkhawa kwambiri?

Tiziyembekezera Kuti Zinthu Zidzakhala Bwino M’tsogolo

N’chifukwa chiyani tinganene kuti malonjezo a m’Baibulo ndi osiyana ndi malonjezo komanso maganizo a anthu?

Kodi Chipembedzo Chasanduka Bizinezi Yotentha?

Nthawi zina anthu amene amabwera kutchalitchi ndi osauka, pomwe m’busa wa tchalitchicho ndi wolemera kwambiri.

Kodi Ndi Ndani Amene Adzapulumutse Dzikoli?

Akatswiri ena a chilengedwe amanena kuti zimene anthu akuchita panopa zikhoza kuwonongeratu mitundu ina ya zinyama ndi zitsamba.

Baibulo Lingathandize Amuna Amene Ali Ndi Nkhawa

Nkhawa ndi vuto lalikulu kwambiri popeza tili munthawi yapadera komanso yovuta, ndiye kodi Baibulo lingakuthandizeni?

Zimene Zingatithandize Ngati Tatopa ndi Mliri

Ngati sitichita zinthu zimene zingatithandize kuti tisatope ndi mliriwu, pang’ono ndi pang’ono tingayambe kugwa ulesi pa nkhani yotsatira malangizo otitetezera ku COVID-19.

Kodi Zinthu Zopanda Chilungamo Zidzatha Padzikoli?

Baibulo limasonyeza kuti chilungamo chenicheni chimachokera kwa Mulungu amene amaona kuti moyo wa munthu aliyense ndi wofunika.

Zimene Zingakuthandizeni Ngati Mwayamba Kudwala Mwadzidzidzi

Kodi ndi mfundo ziti za m’Baibulo zimene zingakuthandizeni ngati mwayamba kudwala mosayembekezereka?

Zimene Mungachite Ngati Mukupeza Ndalama Zochepa

Mavuto azachuma akabwera mwadzidzidzi zimadetsa nkhawa, koma mfundo za m’Baibulo zingakuthandizeni kuti muzitha kugwiritsa ntchito ndalama zochepa.

Mungatani Kuti Musayambe Kumwa Mowa Mopitirira Malire?

Mfundo 5 zimene zingakuthandizeni kuti musamamwe mowa mopitirira malire ngakhale pamene muli ndi nkhawa kwambiri.

Mfundo Zothandiza Anthu Omwe Achitiridwa Nkhanza Zosiyanasiyana

Dziwani kuti wolakwa si inuyo ndipo sikuti muli nokha.

Zimene Mungachite Ngati Muli Nokhanokha

Mukamamva kuti muli nokhanokha, mungayambe kuona kuti simungathe kupeza chiyembekezo, chimwemwe komanso kukhala wokhutira​—komatu si choncho.

NKHANI ZOSIYANASIYANA

Mabuku a Uthenga Wabwino a Mateyu ndi Yohane Atulutsidwa M’Chinenero Chamanja cha ku Germany

Pa 18 December 2021, Mabuku a Uthenga Wabwino a Mateyu ndi Yohane anatulutsidwa m’Chinenero Chamanja cha ku Germany. Kameneka ndi koyamba kuti mabuku athunthu a m’Baibulo atulutsidwe m’chinenerochi.

Uthenga Wotonthoza Anthu Omwe Aferedwa

Munthu amene tinkamukonda akamwalira, tingaganize kuti palibe amene akutimvetsa mmene tikumvera. Koma Mulungu amatimvetsa ndipo ndi wokonzeka kuti atithandize.

Zimene Tingachite Kuti Nsembe ya Yesu Izitithandiza

Kodi Yesu anatiphunzitsa zinthu zofunika ziwiri ziti zimene tiyenera kuchita kuti tipindule ndi imfa yake?

Zimene Mungachite Mukaferedwa

Muone zinthu zimene zingakuthandizeni kupirira.

Baibulo la Dziko Latsopano Lokonzedwanso Linatulutsidwa M’Chisipanishi

Kodi omasulira Baibulo anakwanitsa bwanji kumasulira Baibulo limene mawu amodzi amatanthauza zinthu zingapo m’madera ena apadziko lapansi?

Kodi Yohane M’batizi Anakhalapodi?

Katswiri wolemba mbiri yakale dzina lake Josephus anatsimikizira mfundo yakuti Yohane M’batizi anakhalapodi. Choncho ifenso tiyenera kukhulupirira mfundo imeneyi.

Zolemba Zakale Zimatsimikizira za Malo Amene Aisiraeli Ankakhala

Mapale a ku Samariya amasonyeza kuti zomwe Baibulo limanena zokhudza mbiri yakale ndi zoona.

Kodi Zidindo Zakale Zinkagwira Ntchito Yanji?

N’chifukwa chiyani zidindo zakale zinali zofunika, nanga olamulira ankazigwiritsa ntchito bwanji?

Kodi Zimene Baibulo Limanena Zokhudza Ukapolo wa Ayuda ku Babulo N’zolondola?

Kodi zimene akatswiri ofufuza anapeza zikugwirizana bwanji ndi zimene Mulungu ananena zokhudza moyo wa Ayuda ali ku ukapolo ku Babulo?

Chipilala Chakale cha ku Iguputo Chili Ndi Umboni wa Nkhani ya M’Baibulo

Werengani nkhaniyi kuti muone mmene zolemba zakale za ku Iguputo zimasonyezera kuti anthu omwe analemba Baibulo anali oona mtima.

Mulungu Anapereka Mfundo Zokhudza Ukhondo Asayansi Asanazitulukire

Aisiraeli zinthu zinkawayendera bwino chifukwa chotsatira malangizo a Mulungu okhudza ukhondo.

Zimene Asayansi Afukula Zikutsimikizira Kuti Mfumu Davide Analikodi

Anthu ena amanena kuti Mfumu Davide kunalibe ndipo nkhani yake ndi yongopeka. Kodi asayansi apeza umboni wotani?

Dzina la Mulungu Limapezekanso mu Mpukutu Wakale

Onani umboni wosonyeza kuti dzina la Mulungu linkapezeka mu “Chipangano Chatsopano.”

Njira Zothandiza Powerenga Baibulo

Ndandandayi ingakuthandizeni kwambiri kaya mukufuna kumangowerenga Baibulo tsiku lililonse, kukhala ndi cholinga chomaliza kuwerenga Baibulo chaka chimodzi kapena kutsatira ndondomeko yowerengera Baibulo ya anthu omwe angoyamba kumene.

Kodi Moyo Unayamba Bwanji?

Zoona zake n’zakuti pali anthu ambiri ophunzira kuphatikizapo asayansi ena omwe amakayikira zoti zamoyo zinachita kusintha kuchokera ku zinthu zina.

Mmene Mungapezere Malemba M’Baibulo Lanu

Mndandanda wa mabuku 66 a m’Baibulo ndipo aikidwa mmene aliri m’Mabaibulo ambiri. Dzina la buku lalembedwa koyambirira kenako chaputala ndipo pomaliza vesi lake.

Ankalemekeza Kwambiri Baibulo—Kachigawo ka Vidiyo (William Tyndale)

Umboni wakuti ankakonda kwambiri Baibulo umaonekera mu ntchito imene anagwira imene imatithandizabe masiku ano.

Ankalemekeza Kwambiri Baibulo

William Tyndale komanso Michael Servetus ali m’gulu la anthu omwe ankatsutsidwa komanso kuopsezedwa kuti aphedwa. Iwo analolera kuika moyo wawo pangozi n’cholinga chofuna kuteteza choonadi cha m’Baibulo.

Pepani, palibe mawu ofanana ndi omwe mwasankha