Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Ndimuyandikire

Ndimuyandikire

Pangani Dawunilodi:

  1. 1. Ndinkamva ngati

    Ndilitu ndekhandekha m’chipululu.

    Yehova wanditora

    Ndimam’dalira kwambiri.

    Iye amanditonthoza

    Ndipo ndimamva bwino.

    (KOLASI)

    Ndimuyandikire Yehova

    Andiyandikira.

    An’thandize kuona

    Mmene amandionera.

    Ndimuyandikire.

  2. 2. N’kakumbukira zakale

    Pena ndimadziimba mlandu.

    N’kayamba kumva choncho

    Ndimapemphera pomwepo.

    Yehova amandikonda

    Ndimamva bwinodi.

    (KOLASI)

    Ndimuyandikire Yehova

    Andiyandikira.

    An’thandize kuona

    Mmene amandionera.

    Ndimuyandikire.

    (VESI LOKOMETSERA)

    N’kanapanda kumudziwa

    Ndikanavutika.

    Ndidzadzipereka ndithu

    Mpaka kalekale

    (KOLASI)

    Ndimuyandikire Yehova

    Andiyandikira.

    An’thandize kuona

    Mmene amandionera.

    Ndimuyandikire.